Yakobo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumalakalaka, koma simulandira zimene mukulakalakazo. Mukupitiriza kupha anthu ndiponso mumasirira mwansanje koma simupeza kanthu. Mukupitiriza kukangana komanso kuchita nkhondo.+ Simunalandire chifukwa chakuti simunapemphe. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1998, tsa. 1211/15/1997, tsa. 199/15/1995, tsa. 4
2 Mumalakalaka, koma simulandira zimene mukulakalakazo. Mukupitiriza kupha anthu ndiponso mumasirira mwansanje koma simupeza kanthu. Mukupitiriza kukangana komanso kuchita nkhondo.+ Simunalandire chifukwa chakuti simunapemphe.