Yakobo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,2/1/1999, tsa. 69/1/1998, ptsa. 12-1311/15/1997, ptsa. 19-20
6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+