Yakobo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale, musiye kunenerana zoipa.+ Aliyense amene akunenera zoipa mʼbale wake kapena kumuweruza, akunenera zoipa komanso kuweruza lamulo. Ndiye ngati ukuweruza lamulo, sukuchita zimene lamulo limanena koma ndiwe woweruza. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 20-21
11 Abale, musiye kunenerana zoipa.+ Aliyense amene akunenera zoipa mʼbale wake kapena kumuweruza, akunenera zoipa komanso kuweruza lamulo. Ndiye ngati ukuweruza lamulo, sukuchita zimene lamulo limanena koma ndiwe woweruza.