Yakobo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu Wopereka Malamulo komanso Woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani kuti uziweruza mnzako?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 21
12 Komatu Wopereka Malamulo komanso Woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani kuti uziweruza mnzako?+