Yakobo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Golide ndi siliva wanu wawonongeka ndi dzimbiri. Dzimbiri limenelo lidzakhala umboni wokutsutsani ndipo lidzadya mnofu wanu. Zimene mwasunga zidzakhala ngati moto mʼmasiku otsiriza.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 21-22
3 Golide ndi siliva wanu wawonongeka ndi dzimbiri. Dzimbiri limenelo lidzakhala umboni wokutsutsani ndipo lidzadya mnofu wanu. Zimene mwasunga zidzakhala ngati moto mʼmasiku otsiriza.+