Yakobo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho lezani mtima abale, mpaka kukhalapo kwa Ambuye.+ Ganizirani mmene mlimi amachitira. Iye amayembekezerabe zipatso zamtengo wapatali zochokera munthaka. Amayembekezera moleza mtima mpaka mvula yoyamba komanso mvula yomaliza itagwa.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2023, tsa. 22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2017, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,9/15/2012, tsa. 215/1/1999, tsa. 2411/15/1997, ptsa. 19, 22
7 Choncho lezani mtima abale, mpaka kukhalapo kwa Ambuye.+ Ganizirani mmene mlimi amachitira. Iye amayembekezerabe zipatso zamtengo wapatali zochokera munthaka. Amayembekezera moleza mtima mpaka mvula yoyamba komanso mvula yomaliza itagwa.+
5:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2023, tsa. 22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2017, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,9/15/2012, tsa. 215/1/1999, tsa. 2411/15/1997, ptsa. 19, 22