Yakobo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo cha aneneri amene analankhula mʼdzina la Yehova.*+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:10 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, ptsa. 19-209/15/1994, ptsa. 15-20
10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo cha aneneri amene analankhula mʼdzina la Yehova.*+