Yakobo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma koposa zonse abale anga, siyani kulumbira, potchula kumwamba kapena dziko lapansi kapena lumbiro lina lililonse. Koma mukati “Inde,” azikhaladi inde ndipo mukati “Ayi,” azikhaladi ayi+ kuti musakhale oyenera kuweruzidwa. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:12 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 22
12 Koma koposa zonse abale anga, siyani kulumbira, potchula kumwamba kapena dziko lapansi kapena lumbiro lina lililonse. Koma mukati “Inde,” azikhaladi inde ndipo mukati “Ayi,” azikhaladi ayi+ kuti musakhale oyenera kuweruzidwa.