1 Petulo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inuyo mwabadwanso mwatsopano+ kudzera mʼmawu a Mulungu+ wamoyo ndi wamuyaya. Simunabadwe kuchokera mumbewu yoti ikhoza kuwonongeka, koma mumbewu yomwe singawonongeke.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:23 Nsanja ya Olonda,4/1/2009, tsa. 33/15/1991, tsa. 22
23 Inuyo mwabadwanso mwatsopano+ kudzera mʼmawu a Mulungu+ wamoyo ndi wamuyaya. Simunabadwe kuchokera mumbewu yoti ikhoza kuwonongeka, koma mumbewu yomwe singawonongeke.+