1 Petulo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Poyamba simunali anthu a Mulungu, koma tsopano ndinu anthu ake.+ Mulungu anali asanakuchitireni chifundo, koma tsopano wakuchitirani chifundo.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, tsa. 24
10 Poyamba simunali anthu a Mulungu, koma tsopano ndinu anthu ake.+ Mulungu anali asanakuchitireni chifundo, koma tsopano wakuchitirani chifundo.+