1 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa mʼdzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa kulakalaka zinthu zoipa+ zomwe zili pankhondo yolimbana nanu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,12/15/2012, ptsa. 19, 2111/1/2002, tsa. 12
11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa mʼdzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa kulakalaka zinthu zoipa+ zomwe zili pankhondo yolimbana nanu.+