1 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Antchito azigonjera mabwana awo ndipo aziwalemekeza kwambiri.+ Asamachite zimenezi kwa mabwana abwino ndi ololera okha, koma ngakhalenso kwa ovuta kuwakondweretsa. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Nsanja ya Olonda,2/1/1991, tsa. 21
18 Antchito azigonjera mabwana awo ndipo aziwalemekeza kwambiri.+ Asamachite zimenezi kwa mabwana abwino ndi ololera okha, koma ngakhalenso kwa ovuta kuwakondweretsa.