1 Petulo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ananyamula machimo athu+ mʼthupi lake pamene anamukhomerera pamtengo.+ Anachita zimenezi kuti tipulumutsidwe ku uchimo nʼkumachita zinthu zolungama. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, tsa. 17
24 Iye ananyamula machimo athu+ mʼthupi lake pamene anamukhomerera pamtengo.+ Anachita zimenezi kuti tipulumutsidwe ku uchimo nʼkumachita zinthu zolungama. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+