1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 9 Nsanja ya Olonda,10/15/2002, tsa. 14
12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+