1 Petulo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngakhale mutavutika chifukwa chochita zinthu mwachilungamo, mumakhalabe osangalala.+ Musamaope zimene amaopa* ndipo musamade nazo nkhawa.+
14 Koma ngakhale mutavutika chifukwa chochita zinthu mwachilungamo, mumakhalabe osangalala.+ Musamaope zimene amaopa* ndipo musamade nazo nkhawa.+