1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muzikhala ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti kaya anthu akunenereni zoipa, amene akukunenerani zoipawo adzachite manyazi+ chifukwa cha khalidwe lanu labwino monga otsatira a Khristu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Nsanja ya Olonda,5/1/2003, tsa. 32
16 Muzikhala ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti kaya anthu akunenereni zoipa, amene akukunenerani zoipawo adzachite manyazi+ chifukwa cha khalidwe lanu labwino monga otsatira a Khristu.+