1 Petulo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndi bwino kuvutika chifukwa chochita zabwino,+ ngati Mulungu walola kuti zimenezo zichitike, kusiyana ndi kuvutika chifukwa chochita zoipa.+
17 Ndi bwino kuvutika chifukwa chochita zabwino,+ ngati Mulungu walola kuti zimenezo zichitike, kusiyana ndi kuvutika chifukwa chochita zoipa.+