1 Petulo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pajatu ngakhale Khristu anafa kamodzi kokha kuti achotse uchimo.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama+ kuti akugwirizanitseni ndi Mulungu.+ Iye anaphedwa monga munthu,*+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:18 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 27 Nsanja ya Olonda,2/15/1991, tsa. 15 Kukambitsirana, ptsa. 107-108
18 Pajatu ngakhale Khristu anafa kamodzi kokha kuti achotse uchimo.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama+ kuti akugwirizanitseni ndi Mulungu.+ Iye anaphedwa monga munthu,*+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+
3:18 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 27 Nsanja ya Olonda,2/15/1991, tsa. 15 Kukambitsirana, ptsa. 107-108