1 Petulo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu amenewa adzayankha mlandu kwa Khristu yemwe adzaweruze amoyo ndi akufa omwe.+