1 Petulo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nʼchifukwa chake uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti ngakhale akuweruzidwa malinga ndi mmene akuonekera,* mogwirizana ndi kuona kwa anthu, akhale ndi moyo mwa mzimu mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2008, tsa. 21 Kukambitsirana, ptsa. 205-206
6 Nʼchifukwa chake uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti ngakhale akuweruzidwa malinga ndi mmene akuonekera,* mogwirizana ndi kuona kwa anthu, akhale ndi moyo mwa mzimu mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu.