10 Aliyense wa inu analandira mphatso, choncho muzigwiritsa ntchito mphatso zanuzo potumikirana. Muzichita zimenezi monga atumiki amene amathandiza ena kuti apindule ndi kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene amakusonyeza mʼnjira zosiyanasiyana.+