-
1 Petulo 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ngati wina ali ndi mphatso ya kulankhula, azilankhula mogwirizana ndi mawu opatulika a Mulungu. Ngati wina akutumikira ena, aziwatumikira modalira mphamvu imene Mulungu amapereka.+ Azichita zimenezi kuti Mulungu alemekezeke mʼzinthu zonse+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ulemerero ndi mphamvu ndi zake mpaka muyaya. Ame.
-