1 Petulo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Okondedwa, musadabwe ndi mayesero oyaka moto amene mukukumana nawo+ ngati kuti mukukumana ndi chinachake chachilendo.
12 Okondedwa, musadabwe ndi mayesero oyaka moto amene mukukumana nawo+ ngati kuti mukukumana ndi chinachake chachilendo.