1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma sindikufuna kuti wina wa inu azivutika chifukwa choti wayamba kuba, kupha anthu, kuchita zoipa kapena chifukwa choti akulowerera nkhani za eni.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Nsanja ya Olonda,6/15/1997, ptsa. 30-31
15 Koma sindikufuna kuti wina wa inu azivutika chifukwa choti wayamba kuba, kupha anthu, kuchita zoipa kapena chifukwa choti akulowerera nkhani za eni.+