1 Petulo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati wina akuvutika chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu kwinaku akudziwikabe monga Mkhristu.
16 Koma ngati wina akuvutika chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu kwinaku akudziwikabe monga Mkhristu.