1 Petulo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho amene akuvutika chifukwa choti akuchita zimene Mulungu amafuna, apereke moyo wawo kwa Mlengi wathu amene ndi wokhulupirika nʼkumapitiriza kuchita zabwino.+
19 Choncho amene akuvutika chifukwa choti akuchita zimene Mulungu amafuna, apereke moyo wawo kwa Mlengi wathu amene ndi wokhulupirika nʼkumapitiriza kuchita zabwino.+