2 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukamachita zinthu zonsezi komanso mukamasonyeza kwambiri makhalidwewa, mudzagwiritsa ntchito zinthu zimene mukuzidziwa molondola zokhudza Ambuye wathu Yesu Khristu ndipo zidzakuthandizani kuti musamangokhala kapena kulephera kubereka zipatso.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 118/15/1993, tsa. 17
8 Mukamachita zinthu zonsezi komanso mukamasonyeza kwambiri makhalidwewa, mudzagwiritsa ntchito zinthu zimene mukuzidziwa molondola zokhudza Ambuye wathu Yesu Khristu ndipo zidzakuthandizani kuti musamangokhala kapena kulephera kubereka zipatso.+