2 Petulo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, nʼcholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha. Mukapitiriza kuchita zimenezi, simudzalephera ngakhale pangʼono.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2016, tsa. 19 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, tsa. 219/1/1997, ptsa. 11-124/15/1993, tsa. 28
10 Choncho abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, nʼcholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha. Mukapitiriza kuchita zimenezi, simudzalephera ngakhale pangʼono.+
1:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2016, tsa. 19 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, tsa. 219/1/1997, ptsa. 11-124/15/1993, tsa. 28