2 Petulo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndikuona kuti ndi bwino kuti ndizikugwedezani pokukumbutsani zimenezi+ pamene ndidakali mʼthupi langali, lomwe lili ngati msasa.*+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 12
13 Choncho ndikuona kuti ndi bwino kuti ndizikugwedezani pokukumbutsani zimenezi+ pamene ndidakali mʼthupi langali, lomwe lili ngati msasa.*+