2 Petulo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikuona choncho chifukwa ndikudziwa kuti ndatsala pangʼono kutuluka mumsasa wangawu, mogwirizana ndi mmene Ambuye wathu Yesu Khristu anandiuzira.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 127/15/1993, tsa. 15
14 Ndikuona choncho chifukwa ndikudziwa kuti ndatsala pangʼono kutuluka mumsasa wangawu, mogwirizana ndi mmene Ambuye wathu Yesu Khristu anandiuzira.+