2 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuwonjezera pamenepo, ambiri adzatengera khalidwe lopanda manyazi*+ la aphunzitsi abodzawo ndipo anthu azidzalankhula monyoza njira ya choonadi chifukwa cha aphunzitsiwo.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 14 Mawu a Mulungu, ptsa. 26-27, 32-35
2 Kuwonjezera pamenepo, ambiri adzatengera khalidwe lopanda manyazi*+ la aphunzitsi abodzawo ndipo anthu azidzalankhula monyoza njira ya choonadi chifukwa cha aphunzitsiwo.+