2 Petulo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso mwadyera azidzagwiritsa ntchito mawu achinyengo nʼcholinga choti akudyereni masuku pamutu. Koma chilango chimene Mulungu anakonza kalelo kuti adzawapatse,+ chikubwera mofulumira ndipo chiwonongeko chawo chidzafika ndithu.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 15-169/1/2004, tsa. 159/1/1997, ptsa. 14-153/15/1986, ptsa. 11-12
3 Komanso mwadyera azidzagwiritsa ntchito mawu achinyengo nʼcholinga choti akudyereni masuku pamutu. Koma chilango chimene Mulungu anakonza kalelo kuti adzawapatse,+ chikubwera mofulumira ndipo chiwonongeko chawo chidzafika ndithu.+
2:3 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 15-169/1/2004, tsa. 159/1/1997, ptsa. 14-153/15/1986, ptsa. 11-12