2 Petulo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anawononganso mizinda ya Sodomu ndi Gomora poitentha ndi moto.+ Anachita zimenezi kuti likhale chenjezo kwa anthu osaopa Mulungu la zimene zidzawachitikire mʼtsogolo.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,10/1/2003, ptsa. 20-219/1/1997, tsa. 154/15/1990, ptsa. 16-21
6 Anawononganso mizinda ya Sodomu ndi Gomora poitentha ndi moto.+ Anachita zimenezi kuti likhale chenjezo kwa anthu osaopa Mulungu la zimene zidzawachitikire mʼtsogolo.+