2 Petulo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma anapulumutsa Loti yemwe anali munthu wolungama.+ Loti ankavutika kwambiri mumtima chifukwa cha khalidwe lopanda manyazi* limene anthu ophwanya malamulo ankachita. 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2138 Nsanja ya Olonda,4/15/1990, ptsa. 16-21
7 Koma anapulumutsa Loti yemwe anali munthu wolungama.+ Loti ankavutika kwambiri mumtima chifukwa cha khalidwe lopanda manyazi* limene anthu ophwanya malamulo ankachita.