-
2 Petulo 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 (Munthu wolungamayu ankavutika mumtima tsiku ndi tsiku chifukwa cha zimene ankaona ndiponso kumva pamene ankakhala pakati pa anthu oipa. Iye ankavutika mumtima chifukwa cha zochita zawo zosamvera malamulo.)
-