2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Nsanja ya Olonda,4/15/2012, ptsa. 22-264/15/1990, ptsa. 10-15, 16-21
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+