10 makamaka anthu amene amafunafuna anthu ena nʼcholinga choti awaipitse pogonana nawo+ ndiponso amene amanyoza olamulira.+
Anthu amenewa saopa chilichonse komanso amamva zawo zokha. Iwo sachita mantha kulankhula zinthu zonyoza anthu amene Mulungu wawapatsa ulemerero.