2 Petulo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amalakalaka kwambiri kuchita chigololo*+ komanso amalephera kupewa tchimo, ndipo amakopa anthu achikhulupiriro chosalimba. Ali ndi mtima wophunzitsidwa dyera. Iwo ndi ana otembereredwa. 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 17
14 Amalakalaka kwambiri kuchita chigololo*+ komanso amalephera kupewa tchimo, ndipo amakopa anthu achikhulupiriro chosalimba. Ali ndi mtima wophunzitsidwa dyera. Iwo ndi ana otembereredwa.