2 Petulo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Asocheretsedwa chifukwa anasiya njira yowongoka. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anachita zinthu zoipa chifukwa chofunitsitsa kulandira mphoto,+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 17
15 Asocheretsedwa chifukwa anasiya njira yowongoka. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anachita zinthu zoipa chifukwa chofunitsitsa kulandira mphoto,+