2 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amenewa ndi akasupe opanda madzi komanso nkhungu yotengeka ndi mphepo yamkuntho, ndipo anawasungira mdima wandiweyani.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 18
17 Amenewa ndi akasupe opanda madzi komanso nkhungu yotengeka ndi mphepo yamkuntho, ndipo anawasungira mdima wandiweyani.+