2 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amalankhula mawu odzitukumula opanda pake. Ndipo amagwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso khalidwe lopanda manyazi* pokopa anthu amene angothawa kumene kwa anthu ochita zoipa.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 18
18 Amalankhula mawu odzitukumula opanda pake. Ndipo amagwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso khalidwe lopanda manyazi* pokopa anthu amene angothawa kumene kwa anthu ochita zoipa.+