2 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale kuti akuwalonjeza ufulu, eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Chifukwa aliyense amene wagonjetsedwa ndi winawake, amakhala kapolo wa womugonjetsayo.*+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 18 Galamukani!,4/8/1990, tsa. 14
19 Ngakhale kuti akuwalonjeza ufulu, eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Chifukwa aliyense amene wagonjetsedwa ndi winawake, amakhala kapolo wa womugonjetsayo.*+