2 Petulo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso mʼmatope.”+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, ptsa. 8-9
22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso mʼmatope.”+