2 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo mofanana ndi yoyamba ija, ndikukulimbikitsani kuti muzigwiritsa ntchito bwino mphamvu zanu zoganiza pokukumbutsani zimene mukudziwa kale.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,1/1/2003, ptsa. 9-106/1/1998, tsa. 59/1/1997, tsa. 19
3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo mofanana ndi yoyamba ija, ndikukulimbikitsani kuti muzigwiritsa ntchito bwino mphamvu zanu zoganiza pokukumbutsani zimene mukudziwa kale.+