2 Petulo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amenewa amanyalanyaza mwadala mfundo yakuti, kalero panali kumwamba ndi dziko lapansi lomwe linatuluka mʼmadzi ndi kuima pamwamba pa madziwo chifukwa cha mawu a Mulungu.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,1/1/2013, tsa. 512/15/2006, ptsa. 16-179/1/1997, tsa. 20
5 Anthu amenewa amanyalanyaza mwadala mfundo yakuti, kalero panali kumwamba ndi dziko lapansi lomwe linatuluka mʼmadzi ndi kuima pamwamba pa madziwo chifukwa cha mawu a Mulungu.+