-
2 Petulo 3:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Popeza zinthu zonsezi zidzasungunuka chonchi, ganizirani za mtundu wa anthu amene muyenera kukhala. Muyenera kukhala anthu akhalidwe loyera ndipo muzichita ntchito zosonyeza kuti ndinu odzipereka kwa Mulungu.
-