2 Petulo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho inu okondedwa, popeza mwadziwiratu zimenezi, chenjerani kuti anthu ophwanya malamulowo asakusocheretseni ndi zochita zawo zoipa nʼkuchititsa kuti mugwe chifukwa cholephera kukhala olimba.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,7/15/2010, ptsa. 5, 811/15/2008, tsa. 226/1/1998, tsa. 69/1/1997, tsa. 24
17 Choncho inu okondedwa, popeza mwadziwiratu zimenezi, chenjerani kuti anthu ophwanya malamulowo asakusocheretseni ndi zochita zawo zoipa nʼkuchititsa kuti mugwe chifukwa cholephera kukhala olimba.+