1 Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tikukulemberani zokhudza amene analipo kuyambira pachiyambi, yemwe amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tinamumva ndiponso kumuona ndi maso athu, amene tamuyangʼanitsitsa mwachidwi komanso kumukhudza ndi manja athu. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 26
1 Tikukulemberani zokhudza amene analipo kuyambira pachiyambi, yemwe amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tinamumva ndiponso kumuona ndi maso athu, amene tamuyangʼanitsitsa mwachidwi komanso kumukhudza ndi manja athu.