1 Yohane 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene taziona komanso kuzimva, tikukuuzani+ kuti inunso mugwirizane nafe. Ndipotu ndife ogwirizana ndi Atate ndiponso Mwana wake Yesu Khristu.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, ptsa. 26-27
3 Zimene taziona komanso kuzimva, tikukuuzani+ kuti inunso mugwirizane nafe. Ndipotu ndife ogwirizana ndi Atate ndiponso Mwana wake Yesu Khristu.+