1 Yohane 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tamva uthenga kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu. Uthenga wake ndi wakuti, Mulungu ndiye kuwala+ ndipo kwa iye kulibe mdima ngakhale pangʼono. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,8/1/1991, tsa. 91/15/1987, tsa. 27
5 Ife tamva uthenga kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu. Uthenga wake ndi wakuti, Mulungu ndiye kuwala+ ndipo kwa iye kulibe mdima ngakhale pangʼono.